-
Genesis 11:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako anauzana kuti: “Tiyeni tiumbe njerwa tiziotche.” Atatero, anayamba kumanga ndi njerwa mʼmalo mwa miyala, nʼkumagwiritsa ntchito phula ngati matope omangira.
-