Genesis 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno anati: “Tiyeni timange mzinda wathuwathu, ndipo nsanja yake ikafike mʼmwamba mwenimweni. Tikatero tidzipangira dzina loti titchuke nalo, ndipo sitimwazikana padziko lonse lapansi.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:4 Nsanja ya Olonda,3/15/1998, ptsa. 24-2512/1/1991, tsa. 10
4 Ndiyeno anati: “Tiyeni timange mzinda wathuwathu, ndipo nsanja yake ikafike mʼmwamba mwenimweni. Tikatero tidzipangira dzina loti titchuke nalo, ndipo sitimwazikana padziko lonse lapansi.”+