Genesis 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yehova anati: “Taonani! Izi nʼzimene anthuwa ayamba kuchita, popeza ndi amodzi ndipo onse ali ndi chilankhulo chimodzi.+ Mmene zililimu, angathe kuchita chilichonse chimene akuganiza.
6 Ndiyeno Yehova anati: “Taonani! Izi nʼzimene anthuwa ayamba kuchita, popeza ndi amodzi ndipo onse ali ndi chilankhulo chimodzi.+ Mmene zililimu, angathe kuchita chilichonse chimene akuganiza.