Genesis 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya+ cha nyama iliyonse yamʼtchire padziko lapansi, chamoyo chilichonse chouluka mumlengalenga komanso chokwawa chilichonse chapadziko lapansi chimene chili ndi moyo.” Ndipo zinaterodi.
30 Ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya+ cha nyama iliyonse yamʼtchire padziko lapansi, chamoyo chilichonse chouluka mumlengalenga komanso chokwawa chilichonse chapadziko lapansi chimene chili ndi moyo.” Ndipo zinaterodi.