Genesis 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abulamu anadutsa mʼdzikolo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More.+ Pa nthawiyo nʼkuti Akanani akukhala mʼdzikomo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:6 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 187/1/1989, ptsa. 19-20
6 Abulamu anadutsa mʼdzikolo mpaka kukafika ku Sekemu,+ pafupi ndi mitengo ikuluikulu ya ku More.+ Pa nthawiyo nʼkuti Akanani akukhala mʼdzikomo.