Genesis 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano mʼdzikolo munali njala, ndipo Abulamu ananyamuka kupita ku Iguputo kukakhala kumeneko kwa kanthawi,*+ chifukwa njalayo inafika poipa kwambiri mʼdzikolo.+
10 Tsopano mʼdzikolo munali njala, ndipo Abulamu ananyamuka kupita ku Iguputo kukakhala kumeneko kwa kanthawi,*+ chifukwa njalayo inafika poipa kwambiri mʼdzikolo.+