Genesis 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Mulungu anamaliza kulenga kumwamba ndi dziko lapansi komanso zonse zimene zili mmenemo.+