Genesis 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ngʼombe, abulu aamuna ndi aakazi, antchito aamuna ndi aakazi komanso ngamila.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:16 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, ptsa. 16-178/15/2001, tsa. 21
16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ngʼombe, abulu aamuna ndi aakazi, antchito aamuna ndi aakazi komanso ngamila.+
12:16 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 15 Nsanja ya Olonda,6/15/2011, ptsa. 16-178/15/2001, tsa. 21