Genesis 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Yehova anagwetsera Farao ndi onse amʼbanja lake miliri yoopsa chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:17 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 21
17 Ndiyeno Yehova anagwetsera Farao ndi onse amʼbanja lake miliri yoopsa chifukwa cha Sarai, mkazi wa Abulamu.+