Genesis 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Abulamu anachoka ku Iguputo nʼkulowera ku Negebu.+ Iye anachoka limodzi ndi mkazi wake ndi zonse zimene anali nazo komanso Loti.
13 Choncho Abulamu anachoka ku Iguputo nʼkulowera ku Negebu.+ Iye anachoka limodzi ndi mkazi wake ndi zonse zimene anali nazo komanso Loti.