Genesis 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abulamu atachoka ku Negebu, ankamanga misasa malo osiyanasiyana nʼkumasamuka mpaka anakafika ku Beteli, kumene kunali tenti yake poyamba, pakati pa Beteli ndi Ai.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:3 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 21
3 Abulamu atachoka ku Negebu, ankamanga misasa malo osiyanasiyana nʼkumasamuka mpaka anakafika ku Beteli, kumene kunali tenti yake poyamba, pakati pa Beteli ndi Ai.+