Genesis 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zinapangitsa kuti pabuke mkangano pakati pa abusa a Abulamu ndi abusa a Loti. (Pa nthawiyo nʼkuti Akanani ndi Aperezi akukhala mʼdzikomo.)+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:7 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, ptsa. 21-22
7 Zimenezi zinapangitsa kuti pabuke mkangano pakati pa abusa a Abulamu ndi abusa a Loti. (Pa nthawiyo nʼkuti Akanani ndi Aperezi akukhala mʼdzikomo.)+