-
Genesis 13:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Tiye tisiyane. Ukhoza kusankha mbali iliyonse ya dzikoli. Iwe ukapita kumanzere, ine ndipita kumanja, koma ukapita kumanja, ine ndipita kumanzere.”
-