-
Genesis 2:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7 komanso ananena kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli wakhala akupuma pa ntchito yake yonse. Pamenepa Mulungu anali atamaliza kulenga zinthu zonse zimene ankafuna.
-