Genesis 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Abulamu anapitiriza kukhala mʼdziko la Kanani, koma Loti anakakhala pakati pa mizinda yamʼchigawocho.+ Kenako anakamanga tenti yake pafupi ndi Sodomu. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:12 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 2211/15/1992, ptsa. 13-14
12 Abulamu anapitiriza kukhala mʼdziko la Kanani, koma Loti anakakhala pakati pa mizinda yamʼchigawocho.+ Kenako anakamanga tenti yake pafupi ndi Sodomu.