Genesis 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzachulukitsa mbadwa zako* ngati mchenga wapadziko lapansi. Choncho ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbadwa zako* zidzatha kuwerengedwa.+
16 Ndidzachulukitsa mbadwa zako* ngati mchenga wapadziko lapansi. Choncho ngati munthu angathe kuwerenga mchengawo, ndiye kuti mbadwa zako* zidzatha kuwerengedwa.+