Genesis 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Abulamu anapitiriza kukhala mʼmatenti. Patapita nthawi, anakakhala pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure,+ ku Heburoni.+ Kumeneko, anamangira Yehova guwa lansembe.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:18 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 237/1/1989, tsa. 20
18 Choncho Abulamu anapitiriza kukhala mʼmatenti. Patapita nthawi, anakakhala pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure,+ ku Heburoni.+ Kumeneko, anamangira Yehova guwa lansembe.+