-
Genesis 14:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Pa nthawi imeneyi, mfumu ya ku Sodomu, mfumu ya ku Gomora, mfumu ya ku Adima, mfumu ya ku Zeboyimu, ndi mfumu ya ku Bela, kapena kuti Zowari, ananyamuka nʼkupita ku chigwa cha Sidimu. Kumeneko, iwo anaima mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuti amenyane ndi
-