-
Genesis 14:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Usiku iye anagawa mʼmagulu asilikali akewo, omwe anali atumiki ake, kuti amenyane ndi adaniwo. Ndipo anawagonjetsa, moti anawathamangitsa mpaka kukafika ku Hoba, kumpoto kwa Damasiko.
-