Genesis 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atamandike Mulungu Wamʼmwambamwamba,Amene wapereka okupondereza mʼmanja mwako!” Ndipo Abulamu anapatsa Melekizedeki chakhumi cha zinthu zonse+ zimene analanda adaniwo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:20 Nsanja ya Olonda,7/1/1990, ptsa. 19-20
20 Atamandike Mulungu Wamʼmwambamwamba,Amene wapereka okupondereza mʼmanja mwako!” Ndipo Abulamu anapatsa Melekizedeki chakhumi cha zinthu zonse+ zimene analanda adaniwo.