-
Genesis 14:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Koma Abulamu anauza mfumu ya ku Sodomuyo kuti: “Ndikukweza manja anga kulumbira kwa Yehova Mulungu Wamʼmwambamwamba, Amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi.
-