-
Genesis 14:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndikulumbira kuti pa zinthu zako sinditengapo kanthu nʼkamodzi komwe, ngakhale kaulusi kapena kachingwe komangira nsapato, kuti usadzati, ‘Ndine ndinamulemeretsa Abulamu.’
-