Genesis 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sinditengapo chilichonse kupatulapo zokhazo zimene anyamata adya kale. Koma amene anapita nane, amene ndi Aneri, Esikolo ndi Mamure,+ aliyense akhoza kutenga gawo lake.”
24 Sinditengapo chilichonse kupatulapo zokhazo zimene anyamata adya kale. Koma amene anapita nane, amene ndi Aneri, Esikolo ndi Mamure,+ aliyense akhoza kutenga gawo lake.”