Genesis 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu anayankha kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo Eliezere wa ku Damasiko ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
2 Abulamu anayankha kuti: “Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mudzandipatsa chiyani ine? Taonani ndilibe mwana ndipo Eliezere wa ku Damasiko ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”+