Genesis 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Abulamu ananenanso kuti: “Simunandipatse mwana*+ ndipo mtumiki wanga ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”
3 Abulamu ananenanso kuti: “Simunandipatse mwana*+ ndipo mtumiki wanga ndi amene adzatenge katundu wanga yense monga cholowa chake.”