Genesis 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yehova anamuyankha kuti: “Munthu ameneyu sadzatenga katundu wako monga cholowa chake, koma mwana wako ndi amene adzatenge kuti chikhale cholowa chake.”+
4 Koma Yehova anamuyankha kuti: “Munthu ameneyu sadzatenga katundu wako monga cholowa chake, koma mwana wako ndi amene adzatenge kuti chikhale cholowa chake.”+