-
Genesis 15:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Iye anauza Abulamu kuti: “Utenge ngʼombe yazaka zitatu yomwe sinaberekepo, mbuzi yaikazi yazaka zitatu, nkhosa yamphongo yazaka zitatu, ndiponso njiwa yaingʼono ndi mwana wa nkhunda.”
-