Genesis 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sarai mkazi wa Abulamu, analibe ana.+ Koma iye anali ndi kapolo wake wa ku Iguputo, dzina lake Hagara.+
16 Sarai mkazi wa Abulamu, analibe ana.+ Koma iye anali ndi kapolo wake wa ku Iguputo, dzina lake Hagara.+