-
Genesis 16:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Abulamu atakhala zaka 10 mʼdziko la Kanani, Sarai mkazi wake anapereka Hagara, kapolo wake wa ku Iguputo uja kwa mwamuna wake Abulamu kuti akhale mkazi wake.
-