-
Genesis 16:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Zitatero Abulamu anagona ndi Hagara ndipo iye anakhala woyembekezera. Hagara atazindikira kuti ndi woyembekezera, anayamba kuchitira mwano mbuye wake, Sarai.
-