-
Genesis 16:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Sarai ataona zimenezi anauza Abulamu kuti: “Mlandu wa zimene zikundichitikirazi ukhale pa inu. Ine ndinapereka kapolo wanga kwa inu kuti akhale mkazi wanu, koma iye ataona kuti ndi woyembekezera wayamba kundichitira mwano. Yehova aweruze pakati pa ine ndi inu.”
-