-
Genesis 16:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Abulamu anauza Sarai kuti: “Kapolo wakoyutu ali mʼmanja mwako. Chita chimene ukuchiona kuti nʼchabwino.” Ndiyeno Sarai anayamba kuzunza Hagara, mpaka Hagarayo anathawa.
-