Genesis 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwanayo adzakhala ngati bulu wamʼtchire.* Dzanja lake lidzalimbana ndi aliyense, ndipo dzanja la aliyense lidzalimbana naye. Iye adzakhala pafupi ndi abale ake onse.”*
12 Mwanayo adzakhala ngati bulu wamʼtchire.* Dzanja lake lidzalimbana ndi aliyense, ndipo dzanja la aliyense lidzalimbana naye. Iye adzakhala pafupi ndi abale ake onse.”*