Genesis 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mulungu anapatsa kuwalako dzina lakuti Masana, koma mdimawo anaupatsa dzina lakuti Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali mʼmawa, tsiku loyamba. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
5 Ndiyeno Mulungu anapatsa kuwalako dzina lakuti Masana, koma mdimawo anaupatsa dzina lakuti Usiku.+ Panali madzulo ndiponso panali mʼmawa, tsiku loyamba.