-
Genesis 17:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Abulamu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi. Kenako Mulungu anapitiriza kulankhula naye kuti:
-