Genesis 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndidzasunga pangano limene ine ndachita ndi iwe+ komanso ndi mbadwa zako* mʼmibadwo yawo yonse. Lidzakhala pangano losatha kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbadwa zako.
7 Ndidzasunga pangano limene ine ndachita ndi iwe+ komanso ndi mbadwa zako* mʼmibadwo yawo yonse. Lidzakhala pangano losatha kusonyeza kuti ndine Mulungu wako ndi wa mbadwa zako.