Genesis 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbadwa zako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:8 Galamukani!,5/2012, ptsa. 17-18
8 Dziko limene ukukhalamo ngati mlendoli,+ ndidzalipereka kwa iwe ndi mbadwa zako. Dziko lonse la Kanani lidzakhala lawo mpaka kalekale, ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”+