Genesis 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ mʼmibadwo yanu yonse. Aliyense amene wabadwira mʼnyumba yanu komanso aliyense amene si mbadwa yanu koma munamugula ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.
12 Mwana aliyense wamwamuna amene wakwanitsa masiku 8 azidulidwa+ mʼmibadwo yanu yonse. Aliyense amene wabadwira mʼnyumba yanu komanso aliyense amene si mbadwa yanu koma munamugula ndi ndalama kwa mlendo azidulidwa.