Genesis 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, kenako anayamba kuseka nʼkunena mumtima mwake kuti:+ “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:17 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 14 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, tsa. 21
17 Abulahamu atamva zimenezi anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi, kenako anayamba kuseka nʼkunena mumtima mwake kuti:+ “Kodi mwamuna wa zaka 100 angabereke mwana zoona? Komanso Sara mkazi wa zaka 90, zoona angakhale ndi mwana?”+