Genesis 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake. Adzabereka ana 12 amene adzakhale atsogoleri a mafuko, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+
20 Koma za Isimaeli ndamva pempho lako. Iye ndidzamudalitsa ndipo ndidzamupatsa ana ambiri, komanso ndidzachulukitsa kwambiri mbadwa zake. Adzabereka ana 12 amene adzakhale atsogoleri a mafuko, ndipo ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.+