-
Genesis 2:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Golide wamʼdera limeneli ndi wabwino. Kulinso utomoni wonunkhira wa bedola ndi miyala yamtengo wapatali ya onekisi.
-