Genesis 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Abulahamu anatenga mwana wake Isimaeli ndi amuna onse obadwira mʼnyumba yake, ndi aliyense amene anamugula ndi ndalama zake. Anatenga amuna onse amʼnyumba yake ndipo anawadula tsiku lomwelo monga mmene Mulungu anamuuzira.+
23 Ndiyeno Abulahamu anatenga mwana wake Isimaeli ndi amuna onse obadwira mʼnyumba yake, ndi aliyense amene anamugula ndi ndalama zake. Anatenga amuna onse amʼnyumba yake ndipo anawadula tsiku lomwelo monga mmene Mulungu anamuuzira.+