Genesis 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova+ anaonekera kwa Abulahamu pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure.+ Pa nthawiyi nʼkuti Abulahamu atakhala pansi pakhomo la tenti yake masana dzuwa likuswa mtengo. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 118/1/1991, tsa. 215/15/1988, ptsa. 21-23
18 Kenako Yehova+ anaonekera kwa Abulahamu pakati pa mitengo ikuluikulu ya ku Mamure.+ Pa nthawiyi nʼkuti Abulahamu atakhala pansi pakhomo la tenti yake masana dzuwa likuswa mtengo.
18:1 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 118/1/1991, tsa. 215/15/1988, ptsa. 21-23