Genesis 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Atakweza maso, anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye.+ Atawaona, ananyamuka pakhomo la tentiyo nʼkuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:2 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, tsa. 11
2 Atakweza maso, anaona amuna atatu ataima chapatali ndi iye.+ Atawaona, ananyamuka pakhomo la tentiyo nʼkuthamanga kukakumana nawo. Atafika, anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.