-
Genesis 18:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Popeza mwafika kwa mtumiki wanu, ndiloleni ndikubweretsereni kachakudya kuti mupezenso mphamvu. Kenako mukhoza kupitiriza ulendo wanu.” Pamenepo iwo anati: “Chabwino, chita mmene waneneramo.”
-