Genesis 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Abulahamu anathamangira kutenti kumene kunali Sara nʼkumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu,* uukande nʼkupanga mikate.” Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:6 Nsanja ya Olonda,6/1/2014, tsa. 710/1/1996, tsa. 12
6 Choncho Abulahamu anathamangira kutenti kumene kunali Sara nʼkumuuza kuti: “Fulumira! Tenga ufa wosalala wokwana miyezo itatu,* uukande nʼkupanga mikate.”