-
Genesis 18:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako Abulahamu anathamangira kumene kunali ziweto, nʼkusankha ngʼombe yaingʼono yamphongo yabwino kwambiri. Atatero, anaipereka kwa mtumiki wake, ndipo iye anaikonza mwamsanga.
-