Genesis 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta amumkaka, mkaka ndi ngʼombe yaingʼono yamphongo imene anakonza ija nʼkukaziika pamene panali alendowo. Atatero iye anaimirira chapafupi pa nthawi imene alendowo ankadya atakhala pansi pa mtengo.+
8 Ndiyeno Abulahamu anatenga mafuta amumkaka, mkaka ndi ngʼombe yaingʼono yamphongo imene anakonza ija nʼkukaziika pamene panali alendowo. Atatero iye anaimirira chapafupi pa nthawi imene alendowo ankadya atakhala pansi pa mtengo.+