Genesis 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Sara anayamba kuseka mumtima mwake nʼkunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu komanso mmene mbuyanga wakalambiramu, zoona ndingakhaledi ndi mwayi wobereka mwana?”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:12 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2017, tsa. 14
12 Choncho Sara anayamba kuseka mumtima mwake nʼkunena kuti: “Kodi mmene ndatheramu komanso mmene mbuyanga wakalambiramu, zoona ndingakhaledi ndi mwayi wobereka mwana?”+