Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Ndidzabweranso kwa iwe pa nthawi ngati yomwe ino chaka chamawa, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Ndidzabweranso kwa iwe pa nthawi ngati yomwe ino chaka chamawa, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”